Lirik Lagu Nsokoto The Very Best
Kupata Kwa Ana Iyo Sinkasangalatsidwa Nako
Mwana Apate Eti Tiona Ngati Agone
Chaka Chino Chokha Iye Akagonera Kumanda
M'mati N'kwere Ndakwera Panyumba Yanthakati
Wakoma Bana Pawaka
Wamara Bana Nsokoto
Mwana Akangoti Agone
Kum'bwerera Usiku
Thupi Lonse Lamangika
Kulephera Kufuula
Poti Adsuke Mam'mawa
Thupi Kunjenjemera
Mutu Wanga, Malungo, Matenda Aja Akula
Wakoma Bana
Wati Kitasha
Wamara Bana
Ichi N'chasoni
Nsokoto Nsokoto
Nsokoto Nsokoto
Muuze Nthakatiyo Namulondola Ife Takana
Bana Bakunsokoto Ise
Bana Bakumulowe Ise
Bana Bamwakisulu Ise
Bana Bakaronga Ise
Bana Bakurumphi Ise
Bana Bakuchitipa Ise
post a comment